Ekisodo 29:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Udzatenga masiku 7 poperekera guwa lansembelo nsembe yophimba machimo. Udzaliyeretse+ kuti likhale guwa lansembe loyera koposa.+ Aliyense wokhudza guwa lansembe azikhala woyera.+ Levitiko 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwamuna aliyense+ mwa ana a Aroni azidya mkatewo. Limeneli ndi gawo lawo lochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.+ Chilichonse chimene chingakhudze nsembezi chidzakhala choyera.’”
37 Udzatenga masiku 7 poperekera guwa lansembelo nsembe yophimba machimo. Udzaliyeretse+ kuti likhale guwa lansembe loyera koposa.+ Aliyense wokhudza guwa lansembe azikhala woyera.+
18 Mwamuna aliyense+ mwa ana a Aroni azidya mkatewo. Limeneli ndi gawo lawo lochokera pansembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, m’mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.+ Chilichonse chimene chingakhudze nsembezi chidzakhala choyera.’”