Deuteronomo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Posunga tsiku la sabata ndi kuliona kukhala lopatulika, mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira,+ Yesaya 56:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wodala ndi munthu amene amachita zimenezi,+ ndiponso mwana wa munthu amene amatsatira zimenezi,+ amene amasunga sabata kuti asalidetse,+ ndiponso amaletsa dzanja lake kuti lisachite choipa chilichonse.+
12 “‘Posunga tsiku la sabata ndi kuliona kukhala lopatulika, mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira,+
2 Wodala ndi munthu amene amachita zimenezi,+ ndiponso mwana wa munthu amene amatsatira zimenezi,+ amene amasunga sabata kuti asalidetse,+ ndiponso amaletsa dzanja lake kuti lisachite choipa chilichonse.+