Salimo 106:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odala ndi anthu amene amatsata chilungamo,+Ndi kuchita zolungama nthawi zonse.+ Luka 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma iye anati: “Ayi, m’malomwake, Odala ndi amene akumva mawu a Mulungu ndi kuwasunga!”+