Ekisodo 35:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzigwira ntchito masiku 6,+ koma tsiku la 7 likhale lopatulika kwa inu, likhale sabata la Yehova lopuma pa ntchito zanu zonse. Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli adzaphedwa.+ Numeri 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 M’chipululumo, tsiku lina ana a Isiraeli anapeza munthu wina akutola nkhuni pa tsiku la sabata.+ Numeri 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pambuyo pake Yehova anauza Mose kuti: “Munthuyo aphedwe basi!+ Khamu lonselo likam’ponye miyala kunja kwa msasa.”+
2 Muzigwira ntchito masiku 6,+ koma tsiku la 7 likhale lopatulika kwa inu, likhale sabata la Yehova lopuma pa ntchito zanu zonse. Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli adzaphedwa.+
35 Pambuyo pake Yehova anauza Mose kuti: “Munthuyo aphedwe basi!+ Khamu lonselo likam’ponye miyala kunja kwa msasa.”+