Ekisodo 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muzisunga sabata chifukwa ndi lopatulika kwa inu.+ Amene walinyoza ayenera kuphedwa ndithu.+ Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+ Numeri 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 M’chipululumo, tsiku lina ana a Isiraeli anapeza munthu wina akutola nkhuni pa tsiku la sabata.+ Numeri 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pambuyo pake Yehova anauza Mose kuti: “Munthuyo aphedwe basi!+ Khamu lonselo likam’ponye miyala kunja kwa msasa.”+
14 Muzisunga sabata chifukwa ndi lopatulika kwa inu.+ Amene walinyoza ayenera kuphedwa ndithu.+ Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+
35 Pambuyo pake Yehova anauza Mose kuti: “Munthuyo aphedwe basi!+ Khamu lonselo likam’ponye miyala kunja kwa msasa.”+