Ekisodo 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndipo ana a Isiraeli anachita mogwirizana ndi mawu onse amene Mose anawauza, motero anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala.+
35 Ndipo ana a Isiraeli anachita mogwirizana ndi mawu onse amene Mose anawauza, motero anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala.+