Ekisodo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+ Nehemiya 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene anasungunula chitsulo n’kudzipangira chifanizo cha mwana wa ng’ombe+ n’kuyamba kunena kuti, ‘Uyu ndiye Mulungu wanu, Aisiraeli inu, amene anakutulutsani mu Iguputo,’+ ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani, Salimo 106:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho anasinthanitsa ulemerero wanga+Ndi chifaniziro cha ng’ombe yamphongo yodya udzu.+ Aroma 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 ndipo anasandutsa ulemerero+ wa Mulungu amene sawonongeka kukhala ngati chifaniziro+ cha munthu, mbalame, zolengedwa za miyendo inayi ndi zokwawa,+ zonsezo zimene zimawonongeka.
4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+
18 Pamene anasungunula chitsulo n’kudzipangira chifanizo cha mwana wa ng’ombe+ n’kuyamba kunena kuti, ‘Uyu ndiye Mulungu wanu, Aisiraeli inu, amene anakutulutsani mu Iguputo,’+ ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani,
23 ndipo anasandutsa ulemerero+ wa Mulungu amene sawonongeka kukhala ngati chifaniziro+ cha munthu, mbalame, zolengedwa za miyendo inayi ndi zokwawa,+ zonsezo zimene zimawonongeka.