Ekisodo 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndileke tsopano kuti mkwiyo wanga uwayakire ndipo ndiwafafanize,+ koma iwe ndikupange kukhala mtundu waukulu.”+ Numeri 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Chokani+ pakati pa khamu ili, kuti ndiwafafanize+ kamodzi n’kamodzi.”
10 Ndileke tsopano kuti mkwiyo wanga uwayakire ndipo ndiwafafanize,+ koma iwe ndikupange kukhala mtundu waukulu.”+