14 Sanapemphe thandizo kwa ine ndi mtima wawo wonse+ ngakhale kuti anali kulira mofuula ali pamabedi awo. Anali kungokhala, osachita chilichonse, chifukwa anali ndi chakudya chambiri ndi vinyo wambiri wotsekemera.+ Nthawi zonse anali kuchita zinthu zonditembenukira.+