Oweruza 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno monga mwa masiku onse, iwo analowa m’munda n’kuyamba kukolola ndi kuponda mphesa za m’minda yawo ndi kuchita chikondwerero.+ Kenako analowa m’nyumba ya mulungu wawo,+ ndipo anadya ndi kumwa+ ndi kutemberera+ Abimeleki. Amosi 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo amayala zovala pafupi ndi guwa lililonse lansembe+ ndi kugonapo. Zovala zimenezo zimakhala zimene alanda anthu ena monga chikole.+ Amagula vinyo ndi ndalama zimene alipiritsa anthu ndipo amakamwera vinyoyo kunyumba za milungu yawo.’+
27 Ndiyeno monga mwa masiku onse, iwo analowa m’munda n’kuyamba kukolola ndi kuponda mphesa za m’minda yawo ndi kuchita chikondwerero.+ Kenako analowa m’nyumba ya mulungu wawo,+ ndipo anadya ndi kumwa+ ndi kutemberera+ Abimeleki.
8 Iwo amayala zovala pafupi ndi guwa lililonse lansembe+ ndi kugonapo. Zovala zimenezo zimakhala zimene alanda anthu ena monga chikole.+ Amagula vinyo ndi ndalama zimene alipiritsa anthu ndipo amakamwera vinyoyo kunyumba za milungu yawo.’+