1 Samueli 17:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Choncho iye anafunsa Davide kuti: “Kodi ine ndine galu+ kuti ubwere kwa ine ndi ndodo?” Atatero, anatemberera Davide m’dzina la milungu yake.+ 2 Samueli 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mfumu Davide inafika ku Bahurimu.+ Kumeneko inaona mwamuna wina wa m’banja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera akutuluka ndipo anali kulankhula mawu onyoza.+ Salimo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngati mwakwiya, musachimwe.+Lankhulani mumtima mwanu, muli pabedi panu,+ ndipo mukhale chete. [Seʹlah.] Salimo 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+
43 Choncho iye anafunsa Davide kuti: “Kodi ine ndine galu+ kuti ubwere kwa ine ndi ndodo?” Atatero, anatemberera Davide m’dzina la milungu yake.+
5 Ndiyeno Mfumu Davide inafika ku Bahurimu.+ Kumeneko inaona mwamuna wina wa m’banja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera akutuluka ndipo anali kulankhula mawu onyoza.+
4 Ngati mwakwiya, musachimwe.+Lankhulani mumtima mwanu, muli pabedi panu,+ ndipo mukhale chete. [Seʹlah.]
39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+