Oweruza 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno zinachitika kuti Gidiyoni atangomwalira, ana a Isiraeli anayambanso kupembedza Abaala,+ moti anaika Baala-beriti* kukhala mulungu wawo.+ Oweruza 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako iwo anatenga ndalama zasiliva 70 m’kachisi wa Baala-beriti+ ndi kum’patsa. Ndalama zimenezi Abimeleki analembera ganyu anthu osowa ntchito ndi achipongwe+ kuti azim’tsatira. Oweruza 9:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Nzika zonse za munsanja ya Sekemu zitamva nkhani imeneyi, nthawi yomweyo zinalowa m’chipinda chotetezeka cha m’nyumba ya Eli-beriti.*+
33 Ndiyeno zinachitika kuti Gidiyoni atangomwalira, ana a Isiraeli anayambanso kupembedza Abaala,+ moti anaika Baala-beriti* kukhala mulungu wawo.+
4 Kenako iwo anatenga ndalama zasiliva 70 m’kachisi wa Baala-beriti+ ndi kum’patsa. Ndalama zimenezi Abimeleki analembera ganyu anthu osowa ntchito ndi achipongwe+ kuti azim’tsatira.
46 Nzika zonse za munsanja ya Sekemu zitamva nkhani imeneyi, nthawi yomweyo zinalowa m’chipinda chotetezeka cha m’nyumba ya Eli-beriti.*+