Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 8:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ndiyeno zinachitika kuti Gidiyoni atangomwalira, ana a Isiraeli anayambanso kupembedza Abaala,+ moti anaika Baala-beriti* kukhala mulungu wawo.+

  • Oweruza 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako iwo anatenga ndalama zasiliva 70 m’kachisi wa Baala-beriti+ ndi kum’patsa. Ndalama zimenezi Abimeleki analembera ganyu anthu osowa ntchito ndi achipongwe+ kuti azim’tsatira.

  • Oweruza 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndiyeno monga mwa masiku onse, iwo analowa m’munda n’kuyamba kukolola ndi kuponda mphesa za m’minda yawo ndi kuchita chikondwerero.+ Kenako analowa m’nyumba ya mulungu wawo,+ ndipo anadya ndi kumwa+ ndi kutemberera+ Abimeleki.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena