Ekisodo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho pa tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mamawa, ndi kuyamba kupereka nsembe zopsereza ndi zachiyanjano. Atatero, iwo anakhala pansi ndi kudya ndiponso kumwa. Kenako anaimirira n’kuyamba kusangalala.+ Danieli 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakumwa vinyoyo, iwo anali kutamanda milungu yagolide, yasiliva, yamkuwa, yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala.+ Amosi 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo amayala zovala pafupi ndi guwa lililonse lansembe+ ndi kugonapo. Zovala zimenezo zimakhala zimene alanda anthu ena monga chikole.+ Amagula vinyo ndi ndalama zimene alipiritsa anthu ndipo amakamwera vinyoyo kunyumba za milungu yawo.’+
6 Choncho pa tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mamawa, ndi kuyamba kupereka nsembe zopsereza ndi zachiyanjano. Atatero, iwo anakhala pansi ndi kudya ndiponso kumwa. Kenako anaimirira n’kuyamba kusangalala.+
4 Pakumwa vinyoyo, iwo anali kutamanda milungu yagolide, yasiliva, yamkuwa, yachitsulo, yamitengo ndi yamiyala.+
8 Iwo amayala zovala pafupi ndi guwa lililonse lansembe+ ndi kugonapo. Zovala zimenezo zimakhala zimene alanda anthu ena monga chikole.+ Amagula vinyo ndi ndalama zimene alipiritsa anthu ndipo amakamwera vinyoyo kunyumba za milungu yawo.’+