Amosi 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zovala zimene alanda anthu ena monga chikole,+ amaziyala pafupi ndi guwa lililonse lansembe+ nʼkugonapo.Ndipo vinyo amene amakamwera kunyumba* za milungu yawo, amagula ndi ndalama zimene alipiritsa anthu.’ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, ptsa. 11-12
8 Zovala zimene alanda anthu ena monga chikole,+ amaziyala pafupi ndi guwa lililonse lansembe+ nʼkugonapo.Ndipo vinyo amene amakamwera kunyumba* za milungu yawo, amagula ndi ndalama zimene alipiritsa anthu.’