Amosi 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo amayala zovala pafupi ndi guwa lililonse lansembe+ ndi kugonapo. Zovala zimenezo zimakhala zimene alanda anthu ena monga chikole.+ Amagula vinyo ndi ndalama zimene alipiritsa anthu ndipo amakamwera vinyoyo kunyumba za milungu yawo.’+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, ptsa. 11-12
8 Iwo amayala zovala pafupi ndi guwa lililonse lansembe+ ndi kugonapo. Zovala zimenezo zimakhala zimene alanda anthu ena monga chikole.+ Amagula vinyo ndi ndalama zimene alipiritsa anthu ndipo amakamwera vinyoyo kunyumba za milungu yawo.’+