Oweruza 9:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Atsogoleri onse okhala munsanja ya Sekemu atamva zimenezi, nthawi yomweyo analowa mʼchipinda chotetezeka cha mʼnyumba ya* Eli-beriti.+
46 Atsogoleri onse okhala munsanja ya Sekemu atamva zimenezi, nthawi yomweyo analowa mʼchipinda chotetezeka cha mʼnyumba ya* Eli-beriti.+