Oweruza 9:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Nzika zonse za munsanja ya Sekemu zitamva nkhani imeneyi, nthawi yomweyo zinalowa m’chipinda chotetezeka cha m’nyumba ya Eli-beriti.*+
46 Nzika zonse za munsanja ya Sekemu zitamva nkhani imeneyi, nthawi yomweyo zinalowa m’chipinda chotetezeka cha m’nyumba ya Eli-beriti.*+