Oweruza 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Gidiyoni atangomwalira, Aisiraeli anayambanso kulambira Abaala,+ moti anaika Baala-beriti kukhala mulungu wawo.+ Oweruza 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako iwo anatenga ndalama zasiliva 70 mʼkachisi wa Baala-beriti+ nʼkumupatsa. Ndalama zimenezi Abimeleki analembera ganyu anthu osowa zochita ndi achipongwe kuti azimʼtsatira. Oweruza 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo anapita mʼmunda nʼkukathyola mphesa, kuziponda ndipo kenako anachita chikondwerero. Atatero analowa mʼnyumba ya mulungu wawo+ nʼkuyamba kudya, kumwa ndi kutemberera Abimeleki.
33 Gidiyoni atangomwalira, Aisiraeli anayambanso kulambira Abaala,+ moti anaika Baala-beriti kukhala mulungu wawo.+
4 Kenako iwo anatenga ndalama zasiliva 70 mʼkachisi wa Baala-beriti+ nʼkumupatsa. Ndalama zimenezi Abimeleki analembera ganyu anthu osowa zochita ndi achipongwe kuti azimʼtsatira.
27 Iwo anapita mʼmunda nʼkukathyola mphesa, kuziponda ndipo kenako anachita chikondwerero. Atatero analowa mʼnyumba ya mulungu wawo+ nʼkuyamba kudya, kumwa ndi kutemberera Abimeleki.