Oweruza 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako iwo anatenga ndalama zasiliva 70 mʼkachisi wa Baala-beriti+ nʼkumupatsa. Ndalama zimenezi Abimeleki analembera ganyu anthu osowa zochita ndi achipongwe kuti azimʼtsatira.
4 Kenako iwo anatenga ndalama zasiliva 70 mʼkachisi wa Baala-beriti+ nʼkumupatsa. Ndalama zimenezi Abimeleki analembera ganyu anthu osowa zochita ndi achipongwe kuti azimʼtsatira.