Oweruza 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Gidiyoni atangomwalira, Aisiraeli anayambanso kulambira Abaala,+ moti anaika Baala-beriti kukhala mulungu wawo.+ Oweruza 9:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Atsogoleri onse okhala munsanja ya Sekemu atamva zimenezi, nthawi yomweyo analowa mʼchipinda chotetezeka cha mʼnyumba ya* Eli-beriti.+
33 Gidiyoni atangomwalira, Aisiraeli anayambanso kulambira Abaala,+ moti anaika Baala-beriti kukhala mulungu wawo.+
46 Atsogoleri onse okhala munsanja ya Sekemu atamva zimenezi, nthawi yomweyo analowa mʼchipinda chotetezeka cha mʼnyumba ya* Eli-beriti.+