Ekisodo 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero atayandikira msasawo n’kuona mwana wa ng’ombe+ ndi anthu akuvina, mkwiyo wa Mose unayaka ndipo nthawi yomweyo anaponya pansi miyala ija ndi kuiswa ali m’tsinde mwa phiri.+ Deuteronomo 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo ndinatenga miyala iwiriyo ndi kuiponya pansi mwamphamvu ndi manja anga, ndi kuiswa inu mukuona.+
19 Chotero atayandikira msasawo n’kuona mwana wa ng’ombe+ ndi anthu akuvina, mkwiyo wa Mose unayaka ndipo nthawi yomweyo anaponya pansi miyala ija ndi kuiswa ali m’tsinde mwa phiri.+
17 Pamenepo ndinatenga miyala iwiriyo ndi kuiponya pansi mwamphamvu ndi manja anga, ndi kuiswa inu mukuona.+