Ekisodo 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Popereka magazi a nsembe yanga musawapereke limodzi ndi chilichonse chokhala ndi chofufumitsa. Ndipo mafuta a chikondwerero changa asamagone mpaka m’mawa.+
18 “Popereka magazi a nsembe yanga musawapereke limodzi ndi chilichonse chokhala ndi chofufumitsa. Ndipo mafuta a chikondwerero changa asamagone mpaka m’mawa.+