2 Akorinto 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 osati ngati Mose amene anaphimba nkhope yake ndi nsalu,+ kuti ana a Isiraeli asaone kutha+ kwa ulemerero wosakhalitsawo.
13 osati ngati Mose amene anaphimba nkhope yake ndi nsalu,+ kuti ana a Isiraeli asaone kutha+ kwa ulemerero wosakhalitsawo.