Aroma 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti Khristu ndiye kutha kwa Chilamulo,+ kuti aliyense wokhulupirira akhale wolungama.+