Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri, nsalu zabwino kwambiri, ndi ubweya wa mbuzi.+

  • Ekisodo 26:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Upange nsalu za ubweya wa mbuzi+ zoyala pachihema chopatulika. Upange nsalu 11.

  • Ekisodo 36:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndipo onse a mtima wanzeru+ amene anali kuchita ntchitoyo anayamba kupanga chihema chopatulika,+ nsalu 10 zopetapo akerubi zophimba chihemacho, zopangidwa ndi ulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi ulusi wofiira kwambiri. Iye* anapanga zonsezi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena