Ekisodo 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ulipangire mphete zinayi zagolide ndi kuziika pamwamba pa miyendo yake inayi. Mphete ziwiri zikhale mbali imodzi, ndipo mphete zina ziwiri zikhale mbali inayo.+
12 Ulipangire mphete zinayi zagolide ndi kuziika pamwamba pa miyendo yake inayi. Mphete ziwiri zikhale mbali imodzi, ndipo mphete zina ziwiri zikhale mbali inayo.+