-
Ekisodo 25:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Pamalo atatu a nthambi za mbali imodzi, pakhale masamba ofunga duwa opangidwa ngati maluwa a mtengo wa amondi, ndipo masambawo atsatizane ndi mfundo ndi maluwa. Pamalo atatu a nthambi za mbali inayo, pakhalenso masamba ofunga duwa opangidwa ngati maluwa a mtengo wa amondi, ndipo masambawo atsatizane ndi mfundo ndi maluwa.+ Nthambi 6 zotuluka m’choikapo nyalecho zikhale zotero.
-