Ekisodo 28:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno upise zingwe ziwiri zagolide zija mumphete ziwiri zomwe zili m’makona a chovala pachifuwa.+
24 Ndiyeno upise zingwe ziwiri zagolide zija mumphete ziwiri zomwe zili m’makona a chovala pachifuwa.+