Ekisodo 39:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anapisa zingwe ziwiri zagolide zija m’mphete ziwiri za m’makona a chovala pachifuwa.+ Levitiko 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anamuveka chovala cha pachifuwa+ ndi kuika Urimu ndi Tumimu+ m’chovala cha pachifuwacho.