Ekisodo 28:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kachitsulo kameneko ukamangirire panduwira+ ndi chingwe chabuluu. Kazikhala patsogolo pa nduwirayo.
37 Kachitsulo kameneko ukamangirire panduwira+ ndi chingwe chabuluu. Kazikhala patsogolo pa nduwirayo.