Ekisodo 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno umuveke nduwira pamutu pake ndipo panduwirapo uikepo chizindikiro chopatulika cha kudzipereka.+ Ekisodo 39:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno analowetsa chingwe chabuluu m’kachitsuloko kuti akamangirire panduwirayo,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.
6 Ndiyeno umuveke nduwira pamutu pake ndipo panduwirapo uikepo chizindikiro chopatulika cha kudzipereka.+
31 Ndiyeno analowetsa chingwe chabuluu m’kachitsuloko kuti akamangirire panduwirayo,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.