Ekisodo 29:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho uzipereka ng’ombe ya nsembe yamachimo tsiku ndi tsiku kuti iphimbe machimo.+ Pamenepo uziyeretsa guwa lansembe ku machimo mwa kuliperekera nsembe yophimba machimo, ndipo uzilidzoza+ kuti likhale loyera. Levitiko 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anawaza ena mwa mafuta odzozerawo maulendo 7 paguwa lansembe+ ndi kudzoza guwa lansembelo, zipangizo zake zonse, beseni ndi choikapo chake, n’kuzipatula.
36 Choncho uzipereka ng’ombe ya nsembe yamachimo tsiku ndi tsiku kuti iphimbe machimo.+ Pamenepo uziyeretsa guwa lansembe ku machimo mwa kuliperekera nsembe yophimba machimo, ndipo uzilidzoza+ kuti likhale loyera.
11 Anawaza ena mwa mafuta odzozerawo maulendo 7 paguwa lansembe+ ndi kudzoza guwa lansembelo, zipangizo zake zonse, beseni ndi choikapo chake, n’kuzipatula.