-
Ekisodo 35:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Zinthu zimenezo ndizo chihema chopatulika ndi chophimba chake, ngowe zake, mafelemu ake, mipiringidzo yake, nsanamira zake ndi zitsulo zake zokhazikapo mafelemu ndi mizati.
-