Ekisodo 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Upange nsalu za ubweya wa mbuzi+ zoyala pachihema chopatulika. Upange nsalu 11. Ekisodo 36:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno anapanga nsalu za ubweya wa mbuzi zoyala pachihema chopatulika. Anapanga nsalu 11.+