-
Ekisodo 38:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiyeno nsalu yotchinga pachipata cha bwalo inali yowombedwa mwaluso. Anaiwomba ndi ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+ Inali mikono 20 kutalika kwake, ndipo nsalu yonseyo msinkhu wake unali mikono isanu, mofanana ndi nsalu zotchingira mpanda wa bwalo.+
-