Numeri 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtambowo ukanyamuka pamwamba pa chihemacho, ana a Isiraeli anali kunyamuka nthawi yomweyo.+ Ndipo pamalo pamene mtambowo waima, m’pamene ana a Isiraeli anali kumangapo msasa.+ Numeri 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kaya mtambowo ukhale pamwamba pa chihemacho masiku awiri, mwezi, kapena masiku ambiri, ana a Isiraeli anali kukhalabe pamsasa osachoka. Koma mtambowo ukanyamuka, iwo anali kuchoka.+
17 Mtambowo ukanyamuka pamwamba pa chihemacho, ana a Isiraeli anali kunyamuka nthawi yomweyo.+ Ndipo pamalo pamene mtambowo waima, m’pamene ana a Isiraeli anali kumangapo msasa.+
22 Kaya mtambowo ukhale pamwamba pa chihemacho masiku awiri, mwezi, kapena masiku ambiri, ana a Isiraeli anali kukhalabe pamsasa osachoka. Koma mtambowo ukanyamuka, iwo anali kuchoka.+