Ekisodo 40:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 M’zigawo zonse za ulendo wawo, mtambowo ukakwera pamwamba pa chihema chokumanako, ana a Isiraeli anali kunyamuka n’kuyamba ulendo.+ Numeri 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano m’chaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, pa tsiku la 20,+ mtambo uja unanyamuka pamwamba pa chihema+ cha Umboni. Numeri 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Akanyamuka pamsasa masana, mtambo wa Yehova+ unali pamwamba pawo.
36 M’zigawo zonse za ulendo wawo, mtambowo ukakwera pamwamba pa chihema chokumanako, ana a Isiraeli anali kunyamuka n’kuyamba ulendo.+
11 Tsopano m’chaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, pa tsiku la 20,+ mtambo uja unanyamuka pamwamba pa chihema+ cha Umboni.