Salimo 105:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu anachititsa anthu ake kuberekana,+Ndipo pang’onopang’ono anawasandutsa anthu amphamvu kuposa adani awo.+ Salimo 105:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Aiguputo anasangalala pamene Aisiraeli anatuluka m’dzikolo,Pakuti anali kuwaopa kwambiri.+
24 Mulungu anachititsa anthu ake kuberekana,+Ndipo pang’onopang’ono anawasandutsa anthu amphamvu kuposa adani awo.+