Levitiko 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitatero, Mose anaitana Misayeli ndi Elizafana, ana a Uziyeli,+ bambo aang’ono a Aroni, n’kuwauza kuti: “Bwerani muchotse abale anu patsogolo pa malo oyera, mupite nawo kunja kwa msasa.”+ Numeri 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mtsogoleri wa nyumba ya mabanja a Akohati anali Elizafana, mwana wa Uziyeli.+
4 Zitatero, Mose anaitana Misayeli ndi Elizafana, ana a Uziyeli,+ bambo aang’ono a Aroni, n’kuwauza kuti: “Bwerani muchotse abale anu patsogolo pa malo oyera, mupite nawo kunja kwa msasa.”+