-
Genesis 38:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Ndipo mmene anali kubereka, mwana mmodzi anatulutsa dzanja lake. Nthawi yomweyo mzamba anatenga kachingwe kofiira kwambiri n’kumanga dzanjalo, n’kunena kuti: “Uyu ndiye wayamba kubadwa.”
-