Ekisodo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Yehova anamufunsa kuti: “Chili m’dzanja lakocho n’chiyani?” ndipo Mose anayankha kuti: “Ndodo.”+ Ekisodo 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala+ ndi moto padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala padziko la Iguputo.
2 Pamenepo Yehova anamufunsa kuti: “Chili m’dzanja lakocho n’chiyani?” ndipo Mose anayankha kuti: “Ndodo.”+
23 Ndipo Mose anatambasula dzanja lake ndi kuloza kumwamba ndi ndodo yake. Atatero, Yehova anachititsa mabingu ndipo anagwetsa matalala+ ndi moto padziko lapansi. Choncho Yehova anapitiriza kugwetsa matalala padziko la Iguputo.