Ekisodo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyo, mwamuna wina wa fuko la Levi anakwatira mwana wa Levi.+ Ekisodo 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Awa ndi mayina a ana aamuna a Levi,+ malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo:+ Gerisoni, Kohati ndi Merari.+ Ndipo Levi anakhala ndi moyo zaka 137.
16 Awa ndi mayina a ana aamuna a Levi,+ malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo:+ Gerisoni, Kohati ndi Merari.+ Ndipo Levi anakhala ndi moyo zaka 137.