Ekisodo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Amuramu anatenga Yokebedi, mlongo wa bambo ake, kukhala mkazi wake.+ Ndipo Yokebedi anam’berekera Amuramu, Aroni ndi Mose.+ Amuramu anakhala ndi moyo zaka 137. Numeri 26:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Mkazi wa Amuramu anali Yokebedi,+ mwana wa Levi, amene mkazi wake anam’berekera ku Iguputo. Yokebedi anaberekera Amuramu ana awa: Aroni, Mose ndi mlongo wawo Miriamu.+
20 Tsopano Amuramu anatenga Yokebedi, mlongo wa bambo ake, kukhala mkazi wake.+ Ndipo Yokebedi anam’berekera Amuramu, Aroni ndi Mose.+ Amuramu anakhala ndi moyo zaka 137.
59 Mkazi wa Amuramu anali Yokebedi,+ mwana wa Levi, amene mkazi wake anam’berekera ku Iguputo. Yokebedi anaberekera Amuramu ana awa: Aroni, Mose ndi mlongo wawo Miriamu.+