Ekisodo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyo, mwamuna wina wa fuko la Levi anakwatira mwana wa Levi.+ Ekisodo 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Amuramu anatenga Yokebedi, mlongo wa bambo ake, kukhala mkazi wake.+ Ndipo Yokebedi anam’berekera Amuramu, Aroni ndi Mose.+ Amuramu anakhala ndi moyo zaka 137.
20 Tsopano Amuramu anatenga Yokebedi, mlongo wa bambo ake, kukhala mkazi wake.+ Ndipo Yokebedi anam’berekera Amuramu, Aroni ndi Mose.+ Amuramu anakhala ndi moyo zaka 137.