Machitidwe 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pa nthawi imeneyo Mose anabadwa,+ ndipo anali wokongola kwambiri, ngakhalenso pamaso pa Mulungu.+ Mose analeredwa m’nyumba ya bambo ake kwa miyezi itatu. Aheberi 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwa chikhulupiriro, Mose atabadwa, makolo ake anamubisa kwa miyezi itatu,+ chifukwa anaona kuti mwanayo anali wokongola.+ Iwo sanaope lamulo+ la mfumu.
20 Pa nthawi imeneyo Mose anabadwa,+ ndipo anali wokongola kwambiri, ngakhalenso pamaso pa Mulungu.+ Mose analeredwa m’nyumba ya bambo ake kwa miyezi itatu.
23 Mwa chikhulupiriro, Mose atabadwa, makolo ake anamubisa kwa miyezi itatu,+ chifukwa anaona kuti mwanayo anali wokongola.+ Iwo sanaope lamulo+ la mfumu.