1 Mbiri 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Yuda anali Ere,+ Onani,+ ndi Shela.+ Mwana wamkazi wa Sua Mkanani ndiye anam’berekera ana atatuwa. Ere mwana woyamba wa Yuda anachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo iye anamupha.+ Aheberi 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anatuluka m’fuko la Yuda,+ ndipo ponena za fuko limeneli Mose sanatchulepo chilichonse chokhudza ansembe.
3 Ana a Yuda anali Ere,+ Onani,+ ndi Shela.+ Mwana wamkazi wa Sua Mkanani ndiye anam’berekera ana atatuwa. Ere mwana woyamba wa Yuda anachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo iye anamupha.+
14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anatuluka m’fuko la Yuda,+ ndipo ponena za fuko limeneli Mose sanatchulepo chilichonse chokhudza ansembe.