Ekisodo 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma tirigu*+ sanawonongeke, chifukwa amacha mochedwa. Salimo 105:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Dzombelo linadya zomera zonse m’dziko lawo.+Linadyanso mbewu zonse za m’munda mwawo. Yoweli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Patsogolo pawo moto wawononga+ ndipo kumbuyo kwawo moto walawilawi ukunyeketsa.+ Patsogolo pawo pali dziko ngati la Edeni+ koma kumbuyo kwawo kuli chipululu chowonongeka ndipo palibe chilichonse chopulumuka.
3 Patsogolo pawo moto wawononga+ ndipo kumbuyo kwawo moto walawilawi ukunyeketsa.+ Patsogolo pawo pali dziko ngati la Edeni+ koma kumbuyo kwawo kuli chipululu chowonongeka ndipo palibe chilichonse chopulumuka.