Ekisodo 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo atumiki anu onsewa adzatsika ndi kubwera kwa ine, n’kundigwadira ndi kundiweramira.+ Iwo adzanena kuti, ‘Pita, iweyo ndi anthu onse amene amakutsatira.’ Zitatero ndidzapitadi.” Atanena mawu amenewa anachoka kwa Farao atakwiya. Aheberi 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mwa chikhulupiriro anachoka mu Iguputo,+ koma osati chifukwa choopa mfumu ayi,+ pakuti anapitiriza kupirira moleza mtima ngati kuti akuona Wosaonekayo.+
8 Ndipo atumiki anu onsewa adzatsika ndi kubwera kwa ine, n’kundigwadira ndi kundiweramira.+ Iwo adzanena kuti, ‘Pita, iweyo ndi anthu onse amene amakutsatira.’ Zitatero ndidzapitadi.” Atanena mawu amenewa anachoka kwa Farao atakwiya.
27 Mwa chikhulupiriro anachoka mu Iguputo,+ koma osati chifukwa choopa mfumu ayi,+ pakuti anapitiriza kupirira moleza mtima ngati kuti akuona Wosaonekayo.+