Yoweli 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo achititsa mtengo wanga wa mpesa kukhala chinthu chodabwitsa+ ndipo mtengo wanga wa mkuyu ausandutsa chitsa.+ Nthambi za mitengo imeneyi azichotsa makungwa n’kuzitayira kutali.+ Mphukira zake azichotsa makungwa ndipo zauma. Yoweli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Patsogolo pawo moto wawononga+ ndipo kumbuyo kwawo moto walawilawi ukunyeketsa.+ Patsogolo pawo pali dziko ngati la Edeni+ koma kumbuyo kwawo kuli chipululu chowonongeka ndipo palibe chilichonse chopulumuka.
7 Iwo achititsa mtengo wanga wa mpesa kukhala chinthu chodabwitsa+ ndipo mtengo wanga wa mkuyu ausandutsa chitsa.+ Nthambi za mitengo imeneyi azichotsa makungwa n’kuzitayira kutali.+ Mphukira zake azichotsa makungwa ndipo zauma.
3 Patsogolo pawo moto wawononga+ ndipo kumbuyo kwawo moto walawilawi ukunyeketsa.+ Patsogolo pawo pali dziko ngati la Edeni+ koma kumbuyo kwawo kuli chipululu chowonongeka ndipo palibe chilichonse chopulumuka.